24/08/2026
Every thing GROWS from the ROOTS.
Every nation grows from the grassroots.
The Kwapu Kwapu Nation is growing its grassroots through our Grassroots Partnership Programโcreating opportunities, developing talent, and building the future of football from the ground up.
If you are an Academy or Provincial Team nurturing female football players, we are looking for you.
APPLY NOW.
Contact us: [email protected] | Call/WhatsApp: +260970169123
For God Country And ZISD FC
21/08/2026
Thank you, DStv for the decoder gifts and one-month subscriptions for the Scorchers. ๐บ.
Mphatso iyo! ๐๐พโค๏ธ Ambuye, pitirizani kuwonjezera madalitso anu. Ndine chabe mtsikana waku Ndirande, ndipo mawu ndiribe. Pitirizani kundidalitsa chifukwa cha anzanga ndi banja langa, kuti ndizitha kusintha miyoyo yawo. ๐๐พโค๏ธ
Nambala ni 8.
For God, Country and ZISD FC
21/08/2026
Amu!!!!
For God, Country and ZISD FC
20/08/2026
Tendai Sani and First Lady Professor Gertrude Mutharika at Kamuzu Palace in Lilongwe, Malawi.
Nambala ni 8.
From Ndirande to the World.
Chiuta wa lusungu.
For God, Country and ZISD FC
20/08/2026
aMalawi, kodi mukuwadziwa azibambo awa? Ndi Dolo! ๐ฒ๐ผ๐ฅ
Football Association of Malawi
For God, Country and ZISD FC
20/08/2026
Abwana aFleetwood Haiya. Admin akufunako ka invite aise. ๐ Zingakhale zotentha! Ka Fanta, nkunku ndi rice mwanimana neba. ๐ Tizalindira Christmas. ๐ Zovala zabwino zilipo. Napanga na Londo kale! ๐ฅ
Football Association of Malawi
For God, Country and ZISD FC
19/08/2026
This is a fire picture. Moto ni moto. Scorchers kuti buuuuu. One Neba...Mwacita makora chomene.Mwacita bwino..
18/08/2026
AMalawi, tizibane! ๐ฒ๐ผโค๏ธ
Ikani komwe muli muma comments, monga Ndirande, Blantyre.
Admin akufuna kudyako nsima kwanu. ๐๐
Ndife banja limodzi. We are one Kwapu Kwapu Nation! โค๏ธ๐ฅ
Mpira watibweretsa pamodzi. โฝ๐ฒ๐ผ
For God, Country and ZISD FC
17/08/2026
Congratulations from Zambian Premier League to Tendai Sani.