Msika wogula ndi kugulitsa osewera watsegulidwa lero.
Bungwe loyendetsa masewero a mpira wamiyendo la Fam lalengeza izi kudzera patsamba la mchezo.
Malinga ndi bungweli msikawu udzatsekedwa pa 21 September.
Izi zikutanthauza kuti matimu ali ndi ufulu wogula kapena kugulitsa osewera pakadali pano.
Pakadali pano katswiri wa Blue Eagles Fahad Mcheka komanso Rashid Dah wa Luanar Mitundu ndi ena mwa osewera omwe akufunidwa kwambiri.
Zathuzathu Sports Page
Sangalalani Ndi Zamasewero Zotyakuka Ndi Zathuzathu Sports Page
25/08/2026
FCB Nyasa Big Bullets have signed a 26-year-old Liberian, Sheku Sheriff, from LPRC Oilers on a two-year deal
Maule mwamulandira bwanji katundu ?
22/08/2026
Today's results
21/08/2026
๐จ ๐๐
๐
๐๐๐๐๐: Premier League has confirmed ๐ง๐๐ฐ ๐ซ๐ฎ๐ฅ๐๐ฌ for the 2026/27 season. ๐๐ด๓ ง๓ ข๓ ฅ๓ ฎ๓ ง๓ ฟ
โ
๐๐๐ฐ ๐ซ๐ฎ๐ฅ๐๐ฌ ๐๐๐ข๐ง๐ ๐ข๐ง๐ญ๐ซ๐จ๐๐ฎ๐๐๐:
โฆฟ Injured players must now stay off the pitch for at least ๐ ๐ฆ๐ข๐ง๐ฎ๐ญ๐, up from 30 seconds
โฆฟ A ๐-๐ฌ๐๐๐จ๐ง๐ ๐๐จ๐ฎ๐ง๐ญ๐๐จ๐ฐ๐ง for throw-ins and goal-kicks, with the restart reversed if delayed
โฆฟ Substituted players have just ๐๐ ๐ฌ๐๐๐จ๐ง๐๐ฌ to leave the field, or their replacement waits until the next stoppage
โฆฟ A new VAR review specifically for clearly ๐ฐ๐ซ๐จ๐ง๐ ๐ฌ๐๐๐จ๐ง๐ ๐ฒ๐๐ฅ๐ฅ๐จ๐ฐ cards resulting in a red
โฆฟ A trial requiring managers to nominate an outfield player to leave the pitch for a minute whenever play is stopped for a goalkeeper injury
โ Whatโs ๐ง๐จ๐ญ ๐๐จ๐ฆ๐ข๐ง๐ from this summerโs World Cup:
โฆฟ Hydration breaks
โฆฟ VAR reviews for incorrectly awarded corners
โฆฟ The red-card protocol for players covering their mouths
โฆฟ Yellow cards being reversed for mistaken identity or diving, VAR can only correct who was booked, not the decision itself
๐๐ ๐๐๐ ๐๐๐๐๐ ๐๐๐๐ ๐๐๐ ๐๐๐๐๐๐๐?
20/08/2026
Osewera awiri a Scorchers Tabitha komanso Temwa Chawinga alinawo mu timu ya osewera khumi ndi m'modzi ya Women's Africa Cup of Nations (WAFCON) yomwe bungwe la CAF latulutsa.
Cameroon yomwe inatenga chikhochi itagonjetsa Malawi ili ndi osewera anayi, Algeria yomwe inathera panambala yachitatu ili ndi osewera awiri.
Morocco yomwe inathera panambala yachinayi ilinso ndi awiri.
Zambia yomwe inalephera kufika ndime ya semifainolo ya mpikisanowu ili ndiosewera m'modzi (Babra Banda) pa m'ndandandawu.
CAF yasankha mphunzitsi wa Cameroon Valentine Nguele kuti ndi amene akuphunzitsa timuyi.
17/08/2026
Mphunzitsi wa Scorchers, Lovemore Fazili, wati ndiokondwa kuti alemba mbiri yofika ndime yotsiriza ya Women's Africa Cup of Nations (WAFCON) komanso akwanitsa kudzipezera malo okasewera mu ndime yotsiriza ya Women's World Cup ku Brazil chaka cha mawa.
Fazili wati ngakhale agonja 3-0 dzulo ndi timu ya Cameroon pa bwalo la Moulay El Hassan ku Morocco, apitiriza kuti akhale ndi timu yolimba.
Mphunzitsiyu wati agonja masewerowa kamba koti anachinyitsa zigoli zitatu chigawo choyamba komanso osewera akutsogolo anatchingidwa kwambiri.
Fazili waonjezera kuti osewera ake aonetsa kuti ali ndi kuthekera kopanga zinthu zabwino.
12/08/2026
NBS Bank yalengeza kuti ipeleka K245 million kwa timu ya asungana ya mpira wa miyendo ya Scorchers kamba kokhazikitsa mbiri podzigulira malo ku mpikisano wa 2027 FIFA World Cup mdziko la Brazil.
Mkulu wa NBS Bank a Temwani Simwaka mu uthenga wake madzuro ano, wati izi ndi chilimbikitso kwa osewera, aphunzitsi ndi ena onse omwe akuthandizira asunganawa ku Rabat mdziko la Morroco kuti adzichita bwino.
Izitu zikutanthauza kuti, aliyense mwa anthu 48 omwe ali nu โsquadโ ya Scorchers alandila K7 million kuchoka ku NBS Bank.
Pakadali pano asungwana wa afika ndime yotsiriza ya WAFCON iitapambana 3 - 1 itagonjetsa timu ya Algeria.
12/08/2026
The Malawi national women's football team has reached the final of the CAF Womenโs Africa Cup of Nations in their maiden appearance after a 3-1 victory over Algeria.
The Scorchers delivered a historic performance to book their place in the final, with goals from Tabitha Chawinga, who scored a brace, and Temwa Chawinga sealing the 3-1 win over Algeria.
The result means Malawi has become the first WAFCON debutant to reach the final since the inaugural tournament in 1998. Until now, no debutant had managed the feat.
The Scorchers will now wait to face either hosts Morocco or Cameroon in the final as they chase a first-ever WAFCON title.
10/08/2026
WAKU WORLD CUP -SCORCHERS
Timu ya Scorchers yafika mundime ya semifainolo mumpikisano wa 2026 Women's Africa Cup of Nations itagonjetsa Ghana ndi zigoli ziwiri kwa chimodzi pamasewero omwe anachitikira pa bwalo la Al Madina ku Rabat m'dziko la Morocco.
Temwa Chawinga komanso Rose Kadzere anagoletsera Malawi, pamene Chantelle Boye-Hlorkah anamwetsa chigoli cha Ghana.
Malawi ikumana ndi Algeria pamasewero a ndime ya matimu anayi mumpikisanowu lachitatu pa 12 August 2026.
Kufika mu ndimeyi, Malawi yadzipezera malo ku mpikisano wa 2027 FIFA World Cup omwe udachitikire ku Brazil.
09/08/2026
Today's results
Click here to claim your Sponsored Listing.
Location
Category
Telephone
Website
Address
Pretoria