02/10/2026
Elshadai Chimombo otchinga pagolo wa Chitoliro Heroines walowere ku ZISD FC ku Zambia pa mgwrizano wa zaka zitatu.
Osewerayu yemwe wasewera matimu Monga Dedza Dynamos komanso timu ina ya ku Mozambique, osewera monga Tendai Sani alinso kutimuyi.
Osewerayu waonjezera nambala ya osewera omwe ali mdzikoli ochoka Kumalawi monga Chisomo Banda,Sarah Mlimbika komanso Tendai Sani.
Kwame Angus Nyirongo