27/10/2025
throw back January 5, 2024
SINGINI AKUSAINA CONTRACT YAKE KU MANOMA
Ambiri analankhula pachifukwa chaku munthawi yomwe player yu ankabwera ku timuyi nkuti wanderers ilibe coach aliyense. km pano ndi player odalirika kwambiri ku lali Lubani
27/02/2022
125minutes
Chelsea vs Liverpool
0_0
10/01/2022
1st eleven ya FLAMES
Ernest Kankhobwe
Gomezgan Chirwa
Limbikani Mzava C
Dennis Chembezi
John Banda
Peter Banda
Chimwemwe Idana
Micium Mhone
Francisco Madinga
Khuda Muyaba
Yamikani Chester
07/11/2021
Airtel top8
On 06november
NBB 3 -1 MAFCO
On 7 November
Mighty wanderers 0-1 Moyale barracks
14/04/2021
-resultS
Pa 14 April 2021
Mighty Wanderers 4-1 Ntopwa
Babatunde Hendlix
Wadabwa
Sanudi
Kaliat
05/04/2021
YA FIFA WORLD CUP 2022 QUALIFIERS
Bungwe la mpira wa miyendo pa dziko lonse lapansi FIFA latulutsa ma fixtures ammagulu
Ndipo team ya dzikolino ya flames ili gulu(A) ndi mateam monga Mozambique, Cameroon
05/04/2021
YA FIFA WORLD CUP 2022 QUALIFIERS
Bungwe la mpira wa miyendo pa dziko lonse lapansi FIFA latulutsa ma fixtures ammagulu
Ndipo team ya dzikolino ya flames ili gulu(D) ndi mateam monga Mozambique, Cameroon ndi ena ambiriii
24/01/2021
Man Untd 0-1 Liverpool
19mns {salar}
06/01/2021
ZA MANOMA
.........................................................
Team ya Mighty Wanderers yayambaa zokonzekeraa zake lachiwiri week ino pokonzekeraa
game yomwe alinayo weekend pomwe akhala akusosorana nthengaaa ndi anyamata a Karonga United pa bwaro la KAMUZU STADIUM mu mzindaa wa Blantyre
Ndipo gameyi tizakupasiraniiii LIVE on sports desk(BEN MEKE)
Happy new year all members