Motion Kings Dance Crew

Motion Kings Dance Crew Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from Motion Kings Dance Crew, Dance School, Nsanje.

27/09/2026

Morning famπŸ‡²πŸ‡Όβ€οΈ, nawo ma followers kuzapanga nawo join πŸ˜œπŸ˜‚ thank you so much m guys πŸ”₯πŸ”₯πŸ”₯πŸ”₯πŸ”₯πŸ”₯πŸ”₯

24/09/2026

Good afternoon famβ€οΈπŸ‡²πŸ‡Ό
Tilipano ndinu motion kings dance crew πŸ”₯πŸ”₯πŸ”₯πŸ”₯πŸ”₯

24/09/2026

MORNING FAM❀️. We are here intertaining πŸ”₯πŸ”₯πŸ”₯ Motion kings dance tilipano chifukwa cha support yanu thank you so much πŸ”₯πŸ”₯πŸ”₯πŸ“πŸ™

Morning people tilipano Kukusangalasani komaso ngati Pali ma program amene mukutifuna tipange tiyimbileni phone pa namba...
24/09/2026

Morning people tilipano Kukusangalasani komaso ngati Pali ma program amene mukutifuna tipange tiyimbileni phone pa nambala iyi kuti tinvane ndikukakomesa mwambo wanu πŸ™πŸ”₯πŸ”₯πŸ”₯πŸ”₯πŸ”₯πŸ”₯πŸ”₯

Munthu adzipereka k5,000 yokha bas ndipo adziphunzitsidwa kuyambira Friday mpaka Sunday kenako kujambula limodz ma video...
23/09/2026

Munthu adzipereka k5,000 yokha bas ndipo adziphunzitsidwa kuyambira Friday mpaka Sunday kenako kujambula limodz ma video challenge omwe aphunzira ndikupanga post pa page panoπŸ”₯πŸ”₯πŸ”₯πŸ‡²πŸ‡Ό tiyankhuleni pa nambala iyi kuti mulembetse 0986 06 24 80 anzanu ayamba kale kulembetsa πŸ‡²πŸ‡ΌπŸ”₯πŸ”₯

23/09/2026

Uthenga kwa anthu omwe amatipanga follow. kuyambira Friday likubwerayi tidzikhala tikuphunzitsa anthu kuvina. kwa anthu amene amafunitsitsa kuvina kunsanje kuno tipezeni.Malo ndiomweaja pa MOTA , pafupi ndi nsanje secondary school kapena pafupi ndi nyamnthepa radio station. ndiye kwa omwe akufuna kudzaphunzira, Ife tilipo ndipo mudzatipeza pa MOTA pompo mtengo ndipang'ono bas tidzachita kukambirana .tidziphunzitsa Friday mpaka Sunday masiku atatu amenewo zikomo kwambiri mukafuna kudziwa zambiri tangoyimbani nambala iyi 0894777482 zikomo πŸ™

21/09/2026

Address

Nsanje

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Motion Kings Dance Crew posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Shortcuts

Share

Category