Irenio

Irenio

Share

Irenio is a number1 trusted source for sports news, word's of hope, latest updates and more. Interactive media page

19/08/2026

Takonzeka kusumira Bwede!!!

Anthu ambiri okonda masewera a mpira wamiyendo mziko muno akudzudzula komanso akupempha ochemelera wa timu ya Mighty Wanderers otchedwa Bwede kuti abwere ndi umboni wogwirika pazomwe wanena zokhuza timu ya Bullets...apo ayi iwo akamusumira.

Anthuwa apitiliza kuyankhura kuti; 🎙️-Uku ndikunyazitsa mpira wathu komanso oyendetsa ndi woyimbira kuphatikizapo Football Association yathu...

Ndipo apitiliza kuyankhura kuti "Tiyeni tizitsutsana pa ma team osapotera koma tisaipise mbiri ya team ina...."

Ndipo ena anafunsa kuti 🗣️ Kodi timu yomwe akuinena kuti ndiyabwinoyo, panopa ili pa number yanji ndipo ikusiyana ndi mapoints angati ndi Bullets...koma ngati akunenera umbuli pa mpira tingomumvetsa...

Iwowa atero nanga inuyo kumeneko mukuti bwanji Kodi nkoyenela kuti Bwede akasumilidwe?


19/08/2026

Anthu osiyanasiya afika pabwalo la ndege munzinda wa Lilongwe pamene timu ya dziko lino ya mpira wa miyendo ya Scorchers ikuyembekezeka kufika mdziko muno.

Timuyi ikuyembekezeka kufika nthawi ya 3:30Pm.

Mayi wafuko Mai Gertrude Mutharika akuyembekezeka kufika pabwaloli nthawi Ina iliyonse.

19/08/2026

KODI NKURAKWA KENENA KUTI Mhone Micium NDI OSEWERA OPANDA KHALIDWE?
Paison Oscar Mdoka
MG Malawi
É Måñzêy Sam

19/08/2026

MWASWERA BWANJI MAULE, MA BANKER'S MA EAGLE 🦅 OSAIWARA ANGEREZI! ONLY TOP 4😋

19/08/2026

ZIKOMO YEHOVA POTIPATSA MPHAMVU ZODZUKA NDI MOYO LERO PA 19 AUGUST, MU CHILICHONSE TICHITE LERO MUKHALE KUMBALI YATHU AMEN🙏

19/08/2026

Shout out to our newest followers! Excited to have you onboard! Billy Maupa, Lungu Ngulube Chris, Sam Mitete, Hadrian Kauteme, Anodi Nomal Chee, Anko Layi, Kachoka Chidule Wa Christopher, Peter Watson, Louis Phiri, Satiel Kachepa, Gift Tsokalida, Gray Mpinganjira, Angella Chamakono, Aphique Howah, Gefuly Nyirenda, Elius Bongondo Ngoma, Conscious Kankhuni, Stanly Lozan, Monica Mkomba, Abdul Rashid Wazili Wazili, Masauko Fombe, Mac Maziyaya, Masautso Jilimu, George Mbewe, Edson Khwekhwele, Mandala Pitilosi, Blessings Kabwinja Chibwe, Jones Phiri, Peter Makungwa, Joseph Sosola, Davie J Sakaiko, Henderson Kamoto, Steven Pofera, Peter Tamwa, Brave Ruler, Right Benson, Timatama Chanje, Blasto Uja Ndine, Patrick Mboga, Isaac Mkanthanthama, Haile Banda, Brenda Moyo, Alex Moyenda, Fabrigas Yohani, Ida Chilungu, Joseph Abraham, Justin Jolobala, Hopson Postan, Samuel Chibwana, Moses Anderson.

Let's grow together remember to engage in what ever we share here feel at home 🙏

Admindesk

Photos from Irenio's post 19/08/2026

Tikukuthokozani chifukwa cha chikondi chanu chosatha, ngakhale pamene talakwitsa.

Tikukuthokozani chifukwa cha tsiku la lero. Mulungu, tikupempha chikhululukiro chanu chifukwa tachimwa m’njira zambiri.

Tikupereka tsiku lathu m’manja mwanu, Mulungu Wamphamvuyonse. Tikupempha kuti mukwaniritse zokhumba za mitima yathu.

Bweretsani mtendere m’mitima yathu ndipo mutithandize kuti tikudziweni kwambiri.

Tikupemphani ndi mitima yodzaza ndi chiyamiko.

Tikupemphera m’dzina la Yesu. Ameni! 🙏

🎙️Mtalika

18/08/2026

FT +Champions League

Fenerbahce 1-1 Lyon (HT 0-1)
⚽️Openda 40'(Tolisso)
⚽️Greenwood 47'(Akturkoglu)

18/08/2026

FT Champions League
Levski Sofia 0-0 AEK Athens

Want your business to be the top-listed Gym/sports Facility in Mangochi?

Click here to claim your Sponsored Listing.

Location

Address


Mangochi