31/08/2026
on friday, silver strikers' youth progressed to the finals of FED steel engineering after winning against ascent acadamy at Blue gym ground. wiseman mdumuka scored two goals in the first half to seal the victory.
The finals of the under 19 tournament will be at kaliyeka ground this Sunday.
31/08/2026
Zinthu zikuchitika mwansanga kwambiri.
Pamene inu mmagona, ena anali busy kuimitsana ntchito
30/08/2026
Congratulations Ekhaya football club
MIGHTY WANDRERS FOOTBALL TEAM pepaniiiiiii
30/08/2026
Walero
Airtel top 8 Finals
29/08/2026
Shaq Gwengwe, player yemwe kwawo ndi ku Malawi kuno, ndipo kuthekera Komenya flames ali nako, tsopano wachinya zogoli zitatu pa ma games atatu omwe wasewera ku team yake yatsopano, Newport County Fc mdziko la mangalande.
29/08/2026
Cosafa - Council of Southern Africa Football Associations update
Gaborone 1
Silver 0
60 minutes