24/07/2026
Zomba Chapter!!!
Promoting social capital, interaction and bonding through soccer ⚽⚽.
24/07/2026
Zomba Chapter!!!
16/07/2026
Timathaso kukhwimitsa ubale ndi mabanja, ukwati wa wathuyo timakavina ndithu…
27/06/2026
Amadya ka mtengo!! Ma FC
Since January sitinaluzeko game, tungogawa ma 7 uku ma 6 uku, tumamenyaso ndi masile enawo atagona camp
10/06/2026
Last weekend tinakamenya ndi ka team kenakake kopepuka. Takachinya 7 kwa 1. Nde amabwera ndi yotukwana osadziwa kuti komwe tuchokera iyiyi inali audit course pa Mchinji, tawachinyaso.
Azimenya ndi ana anzawo ku Dedza ko, Weekend yi tikumane pa Golf club.
😂
Team ndi yomweyi inu😂😂
01/05/2026
Munatisowa eti? mwakhaula eti? Tiyeni mawa ku ADL tikachinye JTI! kenako tikaonere super league
24/01/2026
Tayambatu 2026.
Mubwera liti ku team kwathu?