Nkhuku kuti zikule bwino komanso mwa nthanzi zimafunika kuzipatsa ma vitamins osiyanasiyana.
Ku Ziweto Agrovet Shops, tili ndi ma vitamins osiyanasiyana omwe m***a kupeleka ku Nkhuku zanu za lokolo, za nyama komanso za mazira. Mu video iyi alangizi athu akufotokoza zama vitamins omwe timapezeka nawo ku Ziweto Agrovet Shops.
Ziweto Enterprises Limited
ZIWETO ENTERPRISE is a network of franchised agro/vet shops providing veterinary solutions for small
Ziweto is a pioneering company building a unique national network of branded retail outlets (6 to date) selling quality livestock inputs, services and training to livestock farmers across Malawi.
17/08/2026
Dzaleka is open!
16/08/2026
PREDICT & WIN A BRANDED ZIWETO T-SHIRT
Cameroon 🇨🇲 vs Malawi 🇲🇼 ⚽
WAFCON 2026 FINALS
Rules:
1. Follow Ziweto Enterprises. If you already follow us, you can play
2. Comment your exact score after 90 minutes
3. Share this post with others
The first 5 people with the correct score win a Ziweto T-shirts each!
⏰ Entries close today, Sunday 16 August 2026, at 8:30 PM
THE WAIT IS ALMOST OVER!
You guessed it! ZIWETO AGRO-VET SHOP is coming to DZALEKA!
ONLY 2 DAYS TO GO!
We’re excited to bring quality vaccines, veterinary drugs, farm equipment's and animal feed closer to farmers in Dzaleka and surrounding areas.
Dzaleka, get ready! The countdown continues… 🔥
Ziweto Enterprises Limited ZIWETO ENTERPRISE is a network of franchised agro/vet shops providing veterinary solutions for small
13/08/2026
We’re opening a new Ziweto Agrovet Shop, can you guess where?
Tell us the location in the comments.
4 days to go. Stay tuned!
12/08/2026
DAIRY PREMIX
Zipatseni Ng'ombe zanu za mkaka chakudya chabwino chopangidwa ndi Dairy Premix. Dairy premix amathandiza ng’ombe kupanga mkaka wambiri, kugwiritsa ntchito bwino chakudya komanso amathandizanso kupewa matenda oyamba chifukwa chakusowa kwa mavitamini ndi mchere ina.
At Ziweto Enterprises Ltd, we believe practical experience is key to preparing the next generation of agricultural professionals.
We thank the Lilongwe University of Agriculture and Natural Resources students who recently completed their industrial attachment with us for their dedication, professionalism, and commitment throughout the programme. We wish them every success as they apply the knowledge and skills gained to their future careers.
#𝐒𝐤𝐢𝐥𝐥𝐬𝐃𝐞𝐯𝐞𝐥𝐨𝐩𝐦𝐞𝐧𝐭
03/08/2026
SUPER VITAPHOS MAZIWA
Alimi a Ng'ombe za mkaka, zipatseni Ng'ombe zanu michere yofunikila kuti zikhale za thanzi.
VITAPHOS MAZIWA amathandiza kuti:
1. Ng'ombe zizipeleka mkaka ochuluka
2. Ng'ombe zanu zisamagwe zikangobeleka kumene kamba kakusowekela kwa michere ina mthupi
3. Komanso kuti Ng'ombe itenge bele mwachangu ikabeleka
゚viralシ
28/07/2026
Dicalcium Phosphate (DCP) ndi michere yofunika kwambiri mu chakudya cha ziweto monga Ng'ombe, Mbudzi, Nkhumba, Nkhuku ndi zina. DCP amapangisa kuti ziweto zathu zikhale ndi mafupa olimba, kutulutsa mkaka wokhathamila, komanso kuti Nkhuku ziziyikila mazira olimba chikopa mwazina.
゚viralシ
Click here to claim your Sponsored Listing.
Location
Contact the business
Telephone
Website
Address
Malangalanga
Lilongwe
Opening Hours
| Monday | 08:00 - 17:00 |
| Tuesday | 08:00 - 17:00 |
| Wednesday | 08:00 - 17:00 |
| Thursday | 08:00 - 17:00 |
| Friday | 08:00 - 17:00 |
| Saturday | 08:00 - 14:00 |