DRYBORNE SPORT

DRYBORNE SPORT

Share

It's all about sports activities Sports page

30/07/2026

Your Predictions !!!

30/07/2026
Photos from DRYBORNE SPORT's post 30/07/2026

Zotsatira za ena mwa masewero omwe achitika pa Abc Blue Gym

Blu Eagles 3 - 0 Airborne
29. 27
25. 18
25. 21

Midhala 1-3 MIPUNIRO
23. 25
25. 18
22. 25
9. 25

30/07/2026

M & TM CRVL INVITATION TOURNMENT 2026.

BLUE EAGLES VS AIRBORNE

30/07/2026

Mwai Kumwenda Padakali pano ali nawo pa mndandanda wa akatswiri omwe agoletsa ma basiketi ochuluka ku mpikisano wa Commonwealth omwe ukuchitikila m'dziko la Scotland.

Pamasewero asanu omwe timu ya Malawi yasewera katswiriyu wagoletsa ma basiketi 148.

Pa namba 1 pali katswiri wa timu ya Tonga Uneeq Palavi yemwe wagoletsa ma basiketi 170 pamasewero asanu.

30/07/2026

MIDHALA vs MIPUNIRO

Midhala 1-1Mipuniro

20 20

30/07/2026

Masewero a Volleyball akupitilira pa Abc Blue Gym mu nzinda wa Lilongwe mu mpikisano wa M & TM CRVL 2026.

Pamasewero ena amu pool B omwe analipo pakati pa MIDHALA ndi Blantyre Smashers za yenda chonchi.

MIDHALA 3-0 BSM
25. 18
25. 11
25. 22

30/07/2026

M & TM CRVL INVITATION TOURNMENT 2026

NEXT: MIDHALA VS MIPUNIRO

Photos from DRYBORNE SPORT's post 30/07/2026

Yamangana yama Admin a DRYBORNE SPORT pa Blue Gym Court..

@ Obanda 50
@ Leader of Delegation
@ Senior Admin

Photos from DRYBORNE SPORT's post 30/07/2026

Timu ya Malawi the Queen yapeza chipambano chake chachiwiri mu mpikisano wa Glasgow Commonwealth ku Scotland, pomwe ya ngonjetsa Tonga 55-49.

Mu quarter yoyamba Tonga imatsogola 15-14 koma Malawi inasitha zithu mu quarter yachiwiri popita kopumulira Malawi inali ikutsogola ndi ma basiketi 29-26.

-Leader of delagation

Want your business to be the top-listed Gym/sports Facility in Lilongwe?

Click here to claim your Sponsored Listing.

Location

Telephone

Address


Lilongwe