Zochitika mziko

Zochitika mziko

Share

Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from Zochitika mziko, Sport & recreation, Lilongwe.

Profile pictures 27/11/2024

https://www.facebook.com/photo.php?fbid=561408146588721&set=a.140708981991975&type=3&mibextid=rS40aB7S9Ucbxw6v

Panopa ndiye nkhani imene Ili mkamwakamwa ndi yokhuzana ndi mankhwala awa.

Mankhwala amene amadziwika kuti ndi otalikitsa moyo, MA ARV.

Anthu ambiri atutumuka ndi uthenga womwe ukuzungulira mmasamba amchezo woti MA ARV asiya kupangidwa, ndipo ena akuti ma Company opanga mankhwala wa achita kulengezetsa pagulu kuti basi sapanganso ma ARV ena.

Kodi zimenezi ndi zoona? Nanga ndi zoona kuti ma ARV achotsedwa pa ndandanda ya mankhwala amene angatumizidwe ku mayiko ena monga kuno ku Malawi, Zambia ndi mayiko ena?

NKHANI YONSE IFOTOKOZEDWA BWINO LOMWE PABWALO PANO

21/08/2023

Koma kunjaku kukuchitika zinthu 😂

25/07/2023

Interpret the picture 🤷🏼‍♀️🤷🏼‍♀️🤷🏼‍♀️

Want your business to be the top-listed Gym/sports Facility in Lilongwe?

Click here to claim your Sponsored Listing.

Location

Website

Address


Lilongwe