29/08/2026
Chi top fan cha madala Mbiecco emwe aliso mwiniwake kwa ONE LOVE ENTERTAINMENT anati halla inbox at chaisowa music ya fadawa ndiye chati chipanga chilichonse chotheka kuti madalawa atuluse chi track choti tidikulire December akubwelayi
Ati music industry yathu opanda madala Mbiecco sikukoma and iyiyi ndi fact ma up & coming artist ochuluka anapangidwa inspire ndi dolo uyuyu
King Chambiecco ngati muli pa Whatsapp please hit us
29/08/2026
Map challenge apa pokha tikuuzirankoni uku ndikumzimba mwava?
29/08/2026
Mukuchedwa pati this is Long Cee akugawa maticket akufood festival ulele chofunika ndikupanga follow Gist Ya Private Entertainment bas ticket yanu mwaipeza tiyeni
28/08/2026
Sitingakambe za mpira waku Kasungu osatchula dzina la machine awawa
28/08/2026
MALAWIAN TRAVELLER ndiye mpaka lake Kasungu aaaaah ๐๐๐
27/08/2026
Ndiye kuli ichi ulemu wakeso chizilandila
Ayeye Unussu
26/08/2026
Congratulations ma artist omwe asankhidwa kuti akhala mu CENTRAL REGION CYPHER