Follow
LiteraConsult Research Solutions
Scotch at Soccer Show.
The Winning Zone. β½π₯
01/09/2026
For more information follow
LiteraConsult Research Solutions
01/09/2026
01/09/2026
PETER FOTE>CHOMWE CHABAYA BOB MPINGANJIRA NDI TADIKILANI KAYE:
Sanudi ndi Gard Chirwa kumuuza coach kuti mbali iyo siili bwino tithandizeni musinthe kuyankha kwa Bob amangoti tadikilani kaye.
Azake a technical kumuuza Bob mbali iyo ikufunika kusintha kuyankha kwa coach Bob amati tadikilani kaye.
Peter 40 watelo kuti TADIKILANI KAYE wapwetekesa Bob.
Parry Chinyama > Ugonthi wapwetekesa Bob kosafuna kuva zazake ndipo amene uja sabwelelaso ku Malawi kuno timu ikakuyimisa ndi zovuta kuti ubwelele.
Innocent Mphongolo > Timu ya Mighty Wanderers izandikila mochedwa kuti Bob sanayenera kupasa contract koma amasowa pomuyimisila apa apeza chifukwa pomwe aluza ndi Ekhaya Fc. Bob Mpinganjira League yakulila iye uja akuyenera reserve ndikomwe amachita.
Inu maganizo anu ndi otani akutitu uyu sabwelaso ku timu oyimisidwa omwewo azalandila kalata yochoseledwa ali kukhomo.
Pangani follow Wa Mpira Sakwiya kuti muthe kumalandila nkhani zabwino zabwino pano.
01/09/2026
01/09/2026
Zatsimikizika sopano kuti timu ya Mighty Wanderers yasankha mphunzisi wakale wa timu ya dziko lino Patrick Mabedi ngati mlangizi wamkulu wa timuyi (Technical Director)
Malingana ndi zomwe tapeza McDonald Mtetemera ndiye wasankhidwa kukhara mphunzisi oyembekezera wa timuyi kusatira kuchotsedwa Kwa Mphunzisi wamkulu Bob Mpinganjira.
Timu ya Mighty Wanderers FC yachotsa mphunzisi wamkulu wa timuyi kusatira kugonja ndi timu ya Ekhaya FC mpikisano wa Airtel Top 8 pa bwalo la Bingu Stadium
Mukuti wapachibale umenewu πππ
31/08/2026
Mphunzitsi wa might wanderers Bob mpinganjira wasankhidwa ndi Bungwe la football association of Malawi kuti aphunzitsi timu ya Malawi under 23 yomwe isewele ndi ESWATINI mu Africa cup under 23 ndipo opambana azasewela ndi Algeria
Click here to claim your Sponsored Listing.
Location
Contact the business
Telephone
Website
Address
Dowa