Sêñïør³

Sêñïør³

Share

Latest vacancy

05/12/2025

december💔

20/11/2025
20/11/2025

It is well ♥️

Photos from Gwamba's post 20/11/2025
20/11/2025

Tima Harmonize ting'onoting'ono..🙌🙌🙌

I think ndipangitse show uyuyu akhalepo ndizangowauza anthu kuti ndaitana Harmonize Kubangwe! ..🔥🔥

Anyways go and subscribe he's YouTube account!
Watulutsa Nyimbo ndendende Harmonize yo ..

Dzina lake ndi Fredoniah
M***a kumuitanaso kuti Fredonaize mutafuna .😂

Here is the link .

https://youtu.be/gXo22QgnuoQ?si=KrzBTsS5ZB3ROCr0

20/11/2025

kutseka chaka

Zolengeza ndi izi

20/11/2025


Apolisi atsimikiza za kumangidwa kwa m'modzi mwa anthu odziwika bwino ndi nkhani yojambula nyimbo komanso pa masamba a mchezo VJ Ken.

Malingana ndi mneneri wa polisi ya Ndirande a Chibisa Mulimbika, ati VJ Ken yemwe dzina lake ndi Kenneth Makina wa zaka 30, watengedwa pomuganizira kuti amasunga msungwana wa zaka 15 mokakamiza.

A Mulimbika ati mwanayu yemwe wakhala akusowa kuyambira pa 15 November, wapezeka dzulo ndipo wawululula kuti wakhala ali kwa VJ Ken yemwe ndi bwenzi lake.

Apolisi ati mwanayu wawululanso kuti wakhala ali pa ubwenzi ogonana ndi VJ Ken.

(by Innocent Kumchedwa -Lilongwe:11/19/25)

20/11/2025

Woman Crush Wednesday, Ritaa 🔥

Nyimbo Ikhale YOCHOKELA MU Kachikena Album,

Want your business to be the top-listed Gym/sports Facility in Dedza?

Click here to claim your Sponsored Listing.

Location

Address


Chimamba, Linthipe 1
Dedza
KÀPPÀ39