Mphatso The Dream Soccer

Mphatso The Dream Soccer

Share

MPHATSO THE DREAM SOCCER
Is a Community based Juniors Football Club; that develops children and youth with soccer talents.

The Club was founded on
2 August 2024 by a Youth Activist and Social Worker,
Mphatso Limbanga Jr;
The Club is based in Blantyre

19/08/2026
19/08/2026

FIRST LADY ARRIVES AT KIA TO WELCOME THE SCORCHERS πŸ‡²πŸ‡ΌπŸ”₯

Mayi wa Fuko, Gertrude Mutharika, wafika kale pa KIA kudzalandira Scorchers kuchokela Ku WAFCON Morocco. πŸ‡²πŸ‡Όβ€οΈβš½

Welcome home, Queens! πŸ‘‘πŸ”₯
Kwabeba ndikuno

Photos from Mphatso The Dream Soccer's post 18/08/2026

Katswiri otchinga pagolo ku timu ya dziko lino ya Scorchers komanso Civil Service Women's, Mercy Sikelo, watsusa mphekesera zomwe zakhala zikulembedwa pa masamba amchedzo kuti wasiya kusewera mpira ku timu ya dziko lino.

Mtsutsowu wadza pomwe anthu ena akhala akulemba pa masamba amchedzo nkhani zokhuza katswiriyu kuphatikizapo kulemba zoti wasiya kusewera mpira wamiyendo wa asungwana.

Iye wati sakuziwa china chilichonse chokhudza nkhaniyi ndipo wati sanalankhulepo ndi wina aliyense paganizo lake lofuna kusiya kusewera masewero ampira wamiyendo m'dziko muno.

Sikelo ndi m'modzi mwa osewera atimu ya dziko lino omwe athandizira kuti timu ya m'dziko linoyi ichite bwino ku mpikisano wa Women's Africa Cup of Nations WAFCON yomwenso yadzipezera malo kumpikisano wa FIFA Women's World Cup omwe uchitike chaka cha m'mawa m'dziko la Brazil.
Mphatso the Dream Soccer

17/08/2026

Our Queens, Our Heroes πŸ’

16/08/2026

CONGRATULATIONS SCORCHERS !
You have made Malawi Proud ❀️ πŸ‡²πŸ‡Ό
Our Queens Our Heroes

15/08/2026

Go for Glory, Our Queens

Photos from Mphatso The Dream Soccer's post 14/08/2026

Bungwe la akatswiri osewera mpira akale la Football Legends Association (FLA) lati ndikofunikira kwambiri kupereka ulemu kwa osewera a timu ya Scorchers powalola kuti akhale ena mwa mamembala ku bungweri.

Mkulu wa bungweri ,Jim Kalua, wati potengera ndimbiri yabwino yomwe osewerawa achita ku mpikisano wa Women's Africa Cup of Nations (WAFCON) tsopano alowa mu gulu la anthu omwe achitira dziko lino zazikulu pa masewero ampira wamiyendo.

Kalua wayamikira boma komanso Bungwe la Football Association of Malawi (FAM) ,Banki ya National komanso Nthambi yomwe imayendetsa mpira wamiyendo wa asungwana ya National Women's Football Association (NWFA) kamba kokhala ndi chidwi chothandiza timuyi pa nthawi yomwe imakonzekera mpikisanowu.

Scorchers ikumana ndi timu ya Cameron Lamulungu likudzali pa 16 August 2026 pamasewero amundime yotsiliza mumpikisano wa Women's Africa Cup of Nations WAFCON ku Rabat m'dziko la Morocco.

12/08/2026

πŸ‡²πŸ‡ΌπŸ‡²πŸ‡ΌπŸ‡²πŸ‡ΌπŸ‡²πŸ‡ΌπŸ‡²πŸ‡ΌπŸ‡²πŸ‡ΌπŸ‡²πŸ‡ΌπŸ‡²πŸ‡ΌπŸ‡²πŸ‡Ό

11/08/2026

Mphatso The Dream Soccer
is looking for Under-17 Football Players

13/05/2026

Where Legends are Born

Want your business to be the top-listed Gym/sports Facility in Blantyre?

Click here to claim your Sponsored Listing.

Location

Category

Website

Address


Blantyre

Opening Hours

Monday 09:00 - 17:00
Tuesday 09:00 - 17:00
Wednesday 09:00 - 17:00
Thursday 09:00 - 17:00
Friday 09:00 - 17:00
Saturday 09:00 - 17:00