Za Mpira

Za Mpira

Share

Football news from Malawi 🇲🇼 and around the World🌍🗺️⚽🔥🎯 daily updates 🔥

27/08/2026

💥 💥 💣💣

Timu ya FCB Nyasa Big Bullets yalengeza kuti yasaina katswiri womwetsa zigoli wamdziko la Zimbabwe Tinaye Tsimba kukhala wosewera wachiwiri kumusaina pa msika wogula ndi kugulitsa osewera.

Tsimba yemwe ali ndi zaka 23 zakubadwa wasaina mgwirizano wa zaka ziwiri ndi timuyi ndipo akhale akuoneka kutimuyi tsopano.

Osaiwala kupanga follow for more transfer updates 💣⚽

Photos from Za Mpira's post 27/08/2026

Mutakhala Kochi wa Malawi the Flames ndipo muli ndi akatswiri osewera pakati (Defending Midfielders) Atatu koma MUKUFUNA kuyambitsa game mmodzi, wina pa benchi wina mungomtaya palipose!

🟡Lloyd Njaliwa
🟡Aaron Banega Lloyd
🟡Yankho Singo

Mukhoza kupanga motani kuti game muwine?

Osaiwala kupanga follow ⚽

26/08/2026

Shout out to my newest followers! Excited to have you onboard! Chimzy Sungani, Chidakwa Levison Lackson Tomas, Fatuma Best Smooth, Chisomo Kaonga, Kodwani Mauden, Lenadi Nkhoma, Rundu WA Medson Temboh, Blessings Bandah, Yahaya Said, Gift Boy, Josephy Pindan Dilon, Austin Wasopano Sapangwa, Joseph Charles, Andrew Ky Kamnkhwani, Lateefah Hassan, Yohane Wyson Kachingwe, Adams Damzy Kapetuka, Yasoni Nkhoma, Kanyamalibw Ellijah, Ruben Phiri, Thomas kamenya, Keneth C Kadura, Josey MJ Mady, Feristar Kutsanda, Lucas Mangala, Gomezha Mbaly, James Jesnao, Jumullah Jamesd, Buba Mdoka, Wang Xing Chang Feng, Omar Matola, Dingi Gift Luhangas, Malata Precious, Alex Petet, Kanyenda Lucious, Anemwe Ødekha Abalizø, Collings Msenga, Aubameyang Asufant, Bliss Jackson, Vistone Malilo, Lloydmw Namalamba, Chauncy Mlambuzi, Harrison AK Chitsamba, Yesaya Nkoma, Chikafa Leonard, Edward Halla, Fletcher Chande, Gift M Ntanga, Jane Zaipa, Benson Maseko

26/08/2026

🔥 YAFIKILANSO CHIKWATA! 😱⚽🚨

Osewera wa Creck Sporting Club akhoza kuyamba ulendo watsopano ku Blantyre ngati zokambirana zomwe zikuchitika pakati pa FCB Nyasa Big Bullets ndi Creck Sporting zitafika pa mgwirizano. 👀🔥

Zonse zili pa zokambirana pakadali pano, koma Bullets ikuwoneka kuti ikufuna kwambiri osewerayu! 😱💣

Kodi mukuganiza kuti osewerayu angayenerere kuvala jersey ya Bullets? 👇🔥

Osaiwala kupanga follow nkhani zama transfers zingazakuphonyeni🗣️⚽

25/08/2026

Here we go💣💣💥

Team ya Bullets fc yatsindika za kubwera kwa osewera ochokera ku Liberia Sheku Sheriff 🇱🇷

Osaiwala kupanga follow kuti nkhani za masewero zisakuphonyeni ⚽⚽

14/08/2026

After celebrating their 2-0 win over Chitipa United last weekend,FCB Nyasa Big Bullets are heading to Karonga to face Karonga United, will they maintain their momentum?

Osaiwala kupanga follow 🎯⚽

08/08/2026

Big shout out to my newest top fans! Paul B Katunga

01/08/2026

Malawi on 🔥🔥

Highlights ya zigoli zigoli Egypt🇪🇬 1 : 3 Malawi 🇲🇼mbambande⚽⚽⚽

Osaiwala kupanga follow, like, comment and share kuti ma updates ngati awa asamakuphoneni⚽✅💯🔥💪

Want your business to be the top-listed Gym/sports Facility in Blantyre?

Click here to claim your Sponsored Listing.

Location

Website

Address


Blantyre