Mkango ukanyowa susanduka chona. Wandalazi aibabada. Aifwanthamula. Yatuluka ukweche. Ulendo wakukapitolo kukangobwera ndi abitchi, mapikesi, nthoki komanso Uki. Akuterotu dero angoniwo.
Big Bullets Football Club Malawi
Bullets Football Club is the most popular and successful football team in Malawi.It was formed in 19
Celebrating our 14th year on Facebook with a win.Thank you for your continuing support. I could never have made it without you. 🙏🤗🎉
Ulendo waku mangalande anakangophunzira kuliza likweru. Big Bullets Football Club Malawi imaphweka ikakhala sikumenya ndi team Yako.
FT: Mighty Wanderers 1- 2 Nyasa Big Bullets (P.Kamwendo- B.Mpokera, M.G. Phodo)
Ayenda tchibiya tchibiya
Neba Neba Neba Mutu sukugwira
Good morning maule!
Season ya super league ndiye inatha ngakhale sitinamalize mmene tinakakondera , koma still we have Airtel top 8 with in komaso tikuyakba ma games a castle cup.
Tiyeni tipitirirebe kuipatsa moto team.
Click here to claim your Sponsored Listing.
Location
Category
Contact the business
Website
Address
Blantyre
0000