Grandmax Sports Updates

Grandmax Sports Updates

Share

Sports and Recreations

-Sports News Coverage
-Live Football Commentary.

05/08/2026

Basitu Zachitika kuluza ndikudusaso.


05/08/2026

Utha muswedwa pa ground, koma mkupitiraso.

Congratulations ma Scorches athu pomwe mwafika ndime ina ya Women's African Cup of Nations WAFCON

Neba wapela njilu.


05/08/2026

Tikhale tikukuuzani kamba koti tikudikila CAF ibwere ndi chiweluzo chonse kutengela ndi m'mene zayenderamu.


05/08/2026

Full-time

Egypt 2-6 Nigeria


05/08/2026

98'|Goaaaaaaaal!!!!!
Egypt 2-6 Nigeria


05/08/2026

Mawu amodzi a chilimbikitso kwa Asungwana athu!


05/08/2026

8 minutes Added time!!!!

Egypt 2-5 Nigeria


05/08/2026

Osewera komanso akulu-akuku A Scorches akudikira Zotsatira za masewero apakati pa Egypt komanso Nigeria, komatu Nigeria nde ikupambaza 5-2.


05/08/2026

Full-time

Malawi 1-2 Zambia


05/08/2026

Shaaaaah koma abale!!!!

Want your business to be the top-listed Gym/sports Facility in Blantyre?

Click here to claim your Sponsored Listing.

Location

Telephone

Address


Blantyre