17/06/2026
Mighty Wanderers week 7 play of the week its
congratulations 🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉 wapata K300pin kuchoka ku kingbossi motorcycle.
Sports
17/06/2026
Mighty Wanderers week 7 play of the week its
congratulations 🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉 wapata K300pin kuchoka ku kingbossi motorcycle.
16/06/2026
Mongukumbutsana sabata ino ndi ya FDH Bank Premiership ndipo masewero alipo loweruka pa 20 June 2026 pa Mpira/Chiwembe stadium kuyambila nthawi ya 2:30pm.Mighty Wanderers against Ekhaya Fc,monga noma ili pa nkhomo umu ndimene mitengo ya pa gate iliri;
Open stand K10pin
Covered/vip K20pin.
FDH Bank Premiership
💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙
15/06/2026
Fdh Bank premiership yabweranso mu week 7 itapumilidwa Kwa sabata ziwiri kamba ka friendly ya flames ku Ethiopia komanso chinkho cha Airtel top 8.Msabataya nambala 7 wanderers ili pa nkhomo pa chiwembe/mpira stadium pomwe ikhale ikukumana ndi Ekhaya fc kuyambila 2:30pm.Tinakali pa number 1 ndi masewero 7 mapoints 12.
💙
15/06/2026
King Boss player of the week 7 nominations are out.The winners will receive K300pin cash.
Competitors are three players namely
1.Blessings Mwalilino
2.Felix Zulu
3.Dalitso Khungwa
Whom do you vote for???
.
💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙
14/06/2026
At home ?? kunjoya Scottish football ⚽⚽ potsatila Scottish philosophy pamsi pa black Scottish coach
Mtetemera.Kupambana game yoyamba pa khomo next tikupita kwawoko kwa Creck komko.
14/06/2026
Game over
Mighty Wanderers 2-0 Creck Sporting
Blessings Mwalilino 47'
Lameck Mithi 49'
@ mpira stadium
ndiyemwe wasakhidwa kukhala osewera yemwe wasewera bwino kuposa anzake pa game imeneyi.
Congratulations 🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉
.
90+3added
still
Noma 2-0 creck
14/06/2026
Substitute
Adam,Kamanga,kudonto and swilimba in.....
Nahipa,Singini,Kaliati and Nyirenda
out
still
Noma 2-0 Creck
14/06/2026
75minutes
still
Noma 2-0 Creck
nthawi nde ikusendera apa wezwez
14/06/2026
Kubwera wave after wave manoma kufunabe zigoli Zina kuti iduliretu khosi
still
Noma 2-0 Creck
mwalilino 47'
mithi 49'