Welengan mwa chidwi kt munvesese mmene Malawi tapitilila osaiwala kupanga follow page ino
Za overall goal difference zija zimapanga apply pokha pokha ma team awiri akafanana ma point osati mateam atatu.
For example: Zambia ikanakhala ndi 7 points then Malawi and Nigeria 6points ndipomwe za goal difference zija zikanapanga apply.
Koma apapa mu group C mateam onse atatu anali ndi 6points ndekuti sakutengera goal difference koma "mini tournament ya mateam onse atatuwo:
So here is the mini tournament results:
Malawi 3-2 Nigeria
Nigeria 1-0 Zambia
Zambia 2-1 Malawi
Apapa ma game a Egypt sawawerengera
Ndekuti :
Malawi yachinya zigoli 4 (Vs Nigeria, Vs Zambia)
Nigeria yachina zigoli 3 (Vs Malawi, Vs Zambia)
Pomwe Zambia yangochinya zigoli ziwiri (Vs Malawi) basi
Zambia and Egypt atuluka Za masewelo Mchichewa
Za masewelo Mchichewa
Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from Za masewelo Mchichewa, Sports, mondiwadalitso@gmail. com, Blantyre.
We use brain in football ⚽️🇲🇼
Just a single GOAL!
thupi kulemedwa ngt ndi oyembelezera eeeh
05/08/2026
Zambia nayo inve kupweteka lero
Boma la Zambia lapempha asungwana awo kt akuyeneka kuzagonjesa Malawi kuzela kwa nduna yoona za chinyamata ndi masewero chimunya ng'andu poyankhula ndi wailesi ina ya nzokolo wati asungwana a copper queens akuyeneka kuchita chilichonse mmawa kt akwanise kugonjesa Malawi the scorcher
Pangan follow page ino kt zisamakuphonyen Za masewelo Mchichewa
04/08/2026
wapsa wa ku Tanzania Brighton muthali wachoka ku masters walowela ku team ya Mbeya city ya nziko la Tanzania malingana ndi samba la team ya masters ikuthokoza Brighton pa ntchito yabwino yomwe wagwila Ali ku team Yi komanso kumufunila zabwino.
kiti zisamakuphonyen pangan follow page ino Za masewelo Mchichewa
04/08/2026
zathapo masters ndi Khuda atangosewera ma gemu awiri okha asiyanapo kusatila kusanvana ndi coach Peter mponda team yasankha kukhala mbali ya coach ndipo Khuda wavomela kubwenza ndalama zomwe analandila posainila mgwilizano ndi team Yi
pangan follow page ino Za masewelo Mchichewa
03/08/2026
manoma amaoneka ngt alipo ochepa koma anthuwa amabwelesa ka vybe ka chilendo ku mpira wa kuno ku Malawi ndi osamalika anthuwa 😅
mwadzuka bwanji masapota a Nyerere tsiku mwaliyamba bwanji?
09/07/2026
zikhulupiliro ku mpira ichi ndi chithumwa chomwe chatoledwa pa nchima groud Nboma la thyolo pa masewero a Nchima Fc ndi chiladzulu united mu Division 1 Finca mmozi wa chiladzulu united ndi emwe
akuganizilidwa kt wagwesa katunduyi
Follow Za masewelo Mchichewa
Click here to claim your Sponsored Listing.
Location
Category
Website
Address
Mondiwadalitso@gmail. Com
Blantyre