Maule Mwadzuka bwanji lero?
Nyasa Big Bullets The People's Team updates
Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from Nyasa Big Bullets The People's Team updates, Sports, Blantyre.
Maule muli bwanji mutsiku larelo?
05/04/2020
•Continue to Rest in Peace Douglas Section 65 Chirambo
•Patsiko ngati lalero lino mu mchaka cha 2015 pa 5 April ndi tsiku limene katswiri yemwe amasewera mu timu ya Big Bullets komaso Malawi the Flames Douglas Chirambo anamwalira.
•Ndipo lero Douglas Chirambo wakwanitsa zaka 5 ali m'manda
•Mzimu wa Douglas Chirambo upitirize kuwusa muntendere 😭😢
by Dedzaboy (Siddo)
Maule Musamasowe!
Lero tikupwasura timu ya Chicken Inn pa Kamuzu Stadium.
08/02/2020
!!
•Lero kuli chisangalaro ku timu ya Nyasa Big Bullets pomwe katswiri mbambande watimu-yi osewera kumbuyo Charles Petro ali ndi Birthday 🎂
•Charles Petro yemwe pano alimu m'dziko la Moldova kuma trials lero katswiri-yu wakwanitsa zaka 20 zakubadwa....Tiyeni timufunire zabwino katswiri-yu
🎂 Hbd to you CP3 🎉🎉🎉...
by
Dedzaboy (Siddo)
Big Bullets Fc The People's Team 🇦🇹🇦🇹 Squad Travelling To Lilongwe 🚍🚍🚍
_Rabson Chiyenda
_Owen Chaima
____________________
Defenders
_Chirwa Gomez
_Fodya Yamikan
_Zonda Piliran
_Miracle Gabeya
_Bashir Maunde
_Nickson Nyasulu
_Charles Petro
____________________
_*Midfielders
_Chimango Kaila ©_
_Fisher Kondowe
_Henly Kabichi
_Nelson Kangunje
_Righteous Banda
_Ben Manyozo
_Precious Phiri
_Dalitso Sailes
_Chimwemwe Idana
_Mike Mkwate
_Peter Banda
___________________
_Chiukepo Msowoya
_Bright Muthali
_Hassan Kajoke
_Luke Chima
_Patrick Phiri
____________________
Panel
_Kalisto Pasuwa
_Heston Muthali
_Swadick Sanudi
_James Chirapondwa
_Malumbo Chikoko
_Felix Mwalule
_Kimpho Loka
_John Kintu Lanjes
_Precious Sambani
_Ernest Kakhobwe
_Sakhani Mkandawire
The team has just left Blantyre to Lilongwe 🚍🚍🚍
_____________________
Mukawelenga muzitumiza kuma group ena kuti athu ena ajoyine nawo group ino plz
Zeni-zeni
by
✍ Dedzaboy (Siddo )
Nyasa Big Bullets Fc The People's Team 🇦🇹🇦🇹🇦🇹 Today's Training Update @ Blantyre Sports Club ⚽🏃🏻
_Ernest Kakhobwe
_Rabson Chiyenda
____________________
_Sakhani Mkandawire
_Yamikan Fodya
_Piliran Zonda
_Miracle Gabeya
_Bashir Maunde
_Gomez Chirwa
_Nickson Nyasulu
_Charles Petro
____________________
_Chimango Kaila ©
_Fisher Kondowe
_Henly Kabichi
_Nelson Kangunje
_Righteous Banda
_Ben Manyozo
_Macpharlen Ngwira
_Dalitso Sailes
_Chimwemwe Idana
_Mike Mkwate
_Peter Banda
_Ernest Petro
____________________
_Chiukepo Msowoya
_Bright Muthali
_Hassan Kajoke
_Luke Chima
_Patrick Phiri
_____________________
Panel
_Kalisto Pasuwa
_Heston Muthali
_Swadick Sanudi
_James Chirapondwa
_Malumbo Chikoko
_Kimpho Loka
_Felix Mwalule
____________________
Flames U-20 Camp
_Elias Miss
_Mwakifuna Aziz
_Peter Mponda /Coach
_John Lanjes
_Pre Sambani
_Precious Phiri
____________________
••Precious Phiri* sanapange nawo * training lero kamba kakuti dzulo walumidwa ndi *njoka* komano osakhala ndi khawa kweni-kweni *Precious Phiri* akhala akubwelera pa ground chapompano koma *tingomufunira* kuchila mwq msanga 🙏 star wathu-yu.
Musaiwale kupanga forward kuti ena athe kuti joina group ino
____________________
Zeni-zeni
Team Nyasa √⚽🏃🏻
Mighty Tigers Samala??
by Bullets Diehard
Dedzaboy (Siddoo)
Page ino yapangidwa kumene guyz ndiye chofunika mukawelenga muzitumiza kuma group ena kuti athu ena athe kuti joina
🔥❤💪
Click here to claim your Sponsored Listing.
Location
Category
Telephone
Website
Address
Blantyre