08/07/2026
Bola tikukhuta🤣
Sports ⚽⚽
(mr arsenal) 🇲🇼
08/07/2026
Bola tikukhuta🤣
SO FAR!!!!!!!!
✔️Zak*ti Hon Moses Kunkuyu Kalonga Shawa akusunga Black Box zinali zabodza, pak*ti tsopano zadziwika k*ti munalibemo pamene ndege ija inkanyamuka
✓Zachifunga zavomelezedwa k*ti chinalipodi
✓Za capacity ya ndege k*ti ndi 19 koma mipando
ina inachotseswamo k*tsalamo 8 k*ti anyamulire maliro a kasambara zadziwika.
✓Zak*ti achilima ulendo wawo udakonzedwa ndi iwo eni kudzera ku office yawo zadziwikanso
✓Zak*ti a Chimwendo Richard William Banda
adakanizidwa k*ti asakwere malo achepa chifukwa panthawi yo anali anthu ena atatu anali atachotsedwa kale pa list yokwera ndege zadziwikanso
✓Zak*ti Mai Chilima adachita kulephera koma anali nawo pa mndandanda opita ku maliro zadziwikanso
enanu bp ikuchutatu
18/06/2026
report la ndege likuyenda bwino kwambri, okwiyayo amatamba🤣
17/06/2026
anthu mkuyankhula bwanji kodi?
15/06/2026
Gwamba once said ,mmapopana coz mma liva mofanana, 🤣
02/06/2026
cosmo city ext 8 JHB. Anthuwa anawombeledwa usiku wadzuro chamuma 10 usiku, tisamakonde Kuyenda usiku ku dziko la eni💔
26/05/2026
RIP Talumba💔
anthu ambiri aku nkhatabay akupanga post ,zikuonesa kt umacheza bho ndi anthu ,
26/05/2026
munthu uyu anthu akumuthira ma phuzo,
kod walakwisa?
21/05/2026
nde ku malawi kukuchitika drama ili,likazatha mzandikodole
17/05/2026
nako ku nkhatabay ati angoionesa basi eeh, Zimatan k*t mfike pojambulana?