Ndikudikilatu A Noma osatha mpira aja atukwane nde tulo libwela apo bii ine sindisiya Juju Fc😂
Fcb Nyasa Big Bullets Fans
Official page of Fcb Nyasa Big Bullets Fans 🎯
SPORTS CHANNEL📸 MORE UPDATE HERE WE GO
ADMIN NEYMAR 📸🖍️
Mu Fdh mulibe team dzina lake Kapado Fc koma ku Comment itha kupezeka am sure😂 first comment
13/07/2026
MASAKAPENDE SCHOOL GROUND NDI BWALO LIMENE LICHITITSEKO BONAZA YA MA TEAM AKUBALAKA DERA LA MASAKAPENDE TOP 8 BONANZA
MATEAM AKUMANA MOTERE
PA 18 /07/2026 LOWELUKA
NDI VAMPARE VS CHATAMA
NTHAWI YA 3:00 OKOLOK PA BWALO LA MASAKAPENDE GROUND
LAMULUNGU PA 19/07/2026
NDI BLACK LIONS VS ZILOMBO 11 FC
NTHAWI YA 3 OKOLOK MASANA PABWALO LA MASAKAPENDE GROUND LOMWELI
PA 25/07/2026
NDI MASAKAPENDE FC VS SINTHANO FC
NTHAWI YA 3 OKOLOK MASANA PA BWALO LA MASAKAPENDE GROUND
PA 26/07/2026
NDI NAPOLO FC VS AIRTEL FC
NTHAWI YA 3 OKOLOK MASANA PA BWALO LA MASAKAPENDE GROUND
NDIPO MTENGO PAKHOMO NDI ULELE
NDIPO MA TEAM ONSEWA NDI OCHOKELA KWA T/A AMIDU KUBALAKA KOKO
🏟️Malo : masakapende school Ground (balaka).
Mtengo : ndi ulele
Nthawi zina muzikonda kuonera masewero ngati awa kuti muzisiyanitsa ndi osewera mumawapopa aja, m'mderamu muli osewera a luso akungosowa sapoti.
Uuuu ndi wa moto
Anthu Andalama zanu kopita kuika league ndi uku kuli mpira ndipo kuli luso la bwinoko kwambiri ndye Pakufunika kumapanga za support
Ngat mukufuna kumva Zambri imbani or wapu ku number +265 889 61 71 81 NDI 0992007403ndipo muyakhulana ndi modz wa team ya zilombo 11
Fcb Nyasa Big Bullets Fans
Bullets Fans Kodi ndikakamba za noma ndikulakwa?😂
13/07/2026
Levitiko sory sikuti ndi chipongwe kom umagulisa makaka a team iyi kodi imene wavala Bob ilipa zingat i can pay double i want maset aclean
📲Ngati ndapangazi zili ntchimo ndilapa mamawa good night Mighty Angerezi Media
13/07/2026
😂Ndinagona kaya chandizusa ndichani kaya komatu ine zondipasa nkhani ayi Mighty Angerezi Media ndakana
📲Kumwambaku ambiri tikalowa koma kukakhala mafunso anyoi😂😂📲
Fcb Nyasa Big Bullets Fans
13/07/2026
📱Kamega Admin kakuti Good Night Maule🛑⚪
Fcb Nyasa Big Bullets Fans
13/07/2026
📱Mpira umatibwelesa pa modzi ngati Umodzi umodzi wama banker ndipo ngati wachita bwino kapena akuchita bwino zimafunika kuyamikilana ndipo ine ngat mpaletsina ndikufuna kumema masapota nonse a silver strikers Fc komanso ma team onse kuti lets follow Mlakatuli Ericko Mustapher
📱Mzathuyo amaikonda kwambiri team ya silver strikers ndipo akuti ngati afike 10K azapeleka makaka kwa anthu awiri omwe azachite mphumi zikomo
Lets show our love support for Follow him Mlakatuli Ericko Mustapher
New Friend wa Silver tikomese macheza neba akupepuka Follow Mlakatuli Ericko Mustapher
13/07/2026
I like my brother Loyd banrga aroon without any reason
Za nkhani yake sindikufuna kukambanso kali konse chifukwa mwayamba kunditukwanatu
📱What u have to know is this amene timalemba nkhani pa social media tili ndima group omwe timapasana nkhani ndipo timaiunikila tisanalembe pano
📸When u say copy and paste sizimatikhunza kanthu cox we know kuti palibe mukuziwa pa momwe timapezela nkhani zomwe nthawi zonse timalemba pano zikomo??
ndi Admin Fcb Nyasa Big Bullets Fans
Click here to claim your Sponsored Listing.
Location
Category
Address
Cape Town
7100