Cow π Boys 2-1 CAF
π€£
Bwalo La Mapale - Maule Fans
π ππ πππππ πππ πππππππ π πππ πππ'π ππππππ ππππ οΏ½οΏ½ β€οΈβ¨οΈπ₯β¨οΈβ€οΈβ¨οΈπ²πΌπ²πΌπ²πΌοΏ½οΏ½
14/07/2026
π
Tikubwerera ku Mpira Stadium.
Patangopita sabata imodzi kuchokera pamene timakumana mu Airtel Top 8, Tikhale tikubwerera ku Mpira Stadium kukakumana ndi Ekhaya FC mu FDH Bank Premiership.
π Werengani zambiri:https://nyasabigbullets.com/fixtures/ekhaya-next-as-bullets-turn-focus-to-league-response.
Ekhaya next as Bullets turn focus to league response Bullets switch focus back to the FDH Bank Premiership with an away trip to Ekhaya as The People's Team look to extend the unbeaten league run
11/07/2026
π΄ Tsiku la Masewera.
Mphindi zina 90. Malo amodzi mu semifinals.
09/07/2026
LERO NDI TSIKU LIMENE KASWIRI WATHU GEORGE CHAOMBA ANABADWA LET'S WISH HIM A HAPPY BIRTHDAY π
09/07/2026
π NEXT MATCH π
EKHAYA FC
ποΈ MPIRA STADIUM
KICK-OFF TIME 14:30 PM
CONE ON MAULE
04/07/2026
Ndichimenecho maule π₯π₯π₯π₯π₯π₯π₯π₯π₯π₯π₯π₯π₯π₯π₯
Lero chatinyamula ichiiiii Ephraim Kondowe
2 goals kukhalatso man of the match
04/07/2026
KHAAAAAAAAA KHOOOOOOOO
Waishosha FDH Bank PremierShip
Back To Back Wins
03/07/2026
FCB Nyasa Big Bullets Fc Training Update ahead of FDH Bank Premiership Match against Creck Sporting tomorrow at Mpira Stadium
π¦πΉπ¦πΉπ¦πΉπ¦πΉπ¦πΉπ¦πΉπ¦πΉπ¦πΉπ¦πΉπ¦πΉπ¦πΉπ¦πΉπ¦πΉπ¦πΉπ¦πΉπ¦πΉ
GOALKEEPERS
π¦πΉπ¦πΉπ¦πΉπ¦πΉπ¦πΉ
McLean Mwale
Pilirani Mapira
Julius Banda
Innocent Nyasulu
DEFENDERS
π¦πΉπ¦πΉπ¦πΉπ¦πΉπ¦πΉ
Ahmad Kung'unde
Khumbo Banda
Yamikani Mologeni
Aaron Chilipa
Blessings Mpokera (C)
Henry Chiwaya
Edward Thengo
Emanuel Kaunga
Andrew Jovinala
MIDFIELDERS
π¦πΉπ¦πΉπ¦πΉπ¦πΉπ¦πΉ
Yankho Singo
Frank Willard
Chawanangwa Gumbo
Madalitso Safuli
Prince Chiumia
Wongani Lungu
ATTACKERS
π¦πΉπ¦πΉπ¦πΉπ¦πΉπ¦πΉ
Peter Banda
Mike Mkwate
Clever Kalambo
Misheck Billiat
Sean McBrams
STRIKERS
π¦πΉπ¦πΉπ¦πΉπ¦πΉπ¦πΉ
Gasten Phodo
Ephraim Kondowe
Dastan Banda
Hassan Kajoke
George Chaomba
β
Injuries
π¦πΉπ¦πΉπ¦πΉπ¦πΉπ¦πΉ
Paul Master
π― Tineneso pano kuti osewera kumbuyo kwatimuyi Ahmad Kung'unde amene anali ovulala tsopano wachira bwino bwino ndipo wayamba training yamphamvu ndi azinzake. Titsimikizeso pano kuti osewera pakati mutimuyi Madalitso Safuli amene sanasewere nawo sabata yathayi tsopano alibwino ndipo atumikira nawo sabata ino ngati atapatsidwa mpata.
π― Mphunzitsi wamkulu kutimuyi Wedson Wadawada Nyirenda wati akukhulupilira zoti zigoli ziyamba kupezeka zambiri posachedwapa potengera ndimmene osewera akumapangira mipata yomwetsera zigoli. Nyirenda wayankhula izi pamsonkhano wa atolankhani ndipo anapitiliza kunena kuti osewera omwe alipo ndi akungofunika kuwaphunzitsa kudekha akafika malo oti achinye. Wadawada Nyirenda wati pakali pano alimbikitsa osewera omwe ali nawo kaye kuti mipata yogoletsa yambiri yomwe akumapeza aziyigwiritsa ntchito bwino bwino.
β
Tineneso pano kuti mphunzitsiyu yemwe akufunafuna mphangala yoti izimalizitsa ntchito yomwetsa zigoli,wadandaula ndikulephera kusaina Babatunde Adepoju chifukwa amamufuna kwambiri. Nyirenda wati mphunzitsi aliyese amakhala okhumudwa ngati osewera amene amamufuna wapita kutimu kwina komabe ndimmene zimakhalira chifukwa pamapeto pazonse osewera ndamene amasankha komwe akufuna ndipo anapitiliza kunena kuti zateremu ndekuti aponya maso kwa osewera ena amdziko muno komaso kunja kwadziko lino.
π Wadawada Nyirenda wapereka ulemu kwa masapota a Bullets amene wati amuonetsera chikondi lolemba lapitali pa Mpira Stadium pomwe anamuyitana kuti akamupatse moni. Nyirenda wati zimenezi ndizofunikira kwambiri chifukwa zamulimbikitsa kwambiri ndipo anati sapota amafuna kupambana nthawi zonse kotero kuti alimbikitsa osewera ake kuti ayikilepo mtima chifukwa masapota amalipira ndalama pageti kuti awone timu yawo ikupambana...
ποΈ Masana abwino Mapale kulikonse komwe muli ndimakunyadirani kwambiri. Ine ndiyemwe uja die hard wamkulu.
ποΈ
Maule4Life β€οΈ β½ β
π―π―π―π―π―π―π―π―
30/06/2026
Wada Wada πͺπ»πͺπ»
Mau amodzi maule
30/06/2026
Frank Willard is back, ichichi kungoti ma injury amangochivuta koma ndi akatundu.
Malo aja chatenga ndipo dzulo chagaza mpira osat masewera.
Click here to claim your Sponsored Listing.
Location
Category
Website
Address
ZIP