29/08/2026
Happy Birthday to our team Captain! ππ
A true leader on and off the field, your commitment, discipline, and passion continue to inspire the entire team. May this year bring you strength, success, and many more victories.
Enjoy your day, we appreciate you!
π
26/08/2026
Our Home Ground
ποΈ Jenda Community Ground
Sapoti yanu nthawi zonse timayinyadira tiyeni tikumane Lamulungu(30/8/2026)
π
25/08/2026
πππ ππππ πππππ
π:
β½οΈ: Jenda UnitedπChihame All Stars
π Sunday, 30 August 2026
π: Jenda Community Ground
π : 2:30 PM
π΄π
24/08/2026
ππ‘π’πͺ π¬π’π¨π₯ π£πππ¬ππ₯π¦
CHISOMO NATHAN MYEGHA
Position: Midfielder
Nationality: Malawi
Age: 18
Jersey No: 19
Iyii ndi yake yoyamba kumenya chikho chachikulu mu chigawo chaku mpoto.
Pakadali pano ali ndi zigoli ziwiri pamasewero seven omwe wasewera mu chikho cha Chiwemi Investment NRFA League One .
π
21/08/2026
PAINFUL DEFEAT
Tikupepetsa kwama sapota athu nonse kuti lero zithu sizinayende momwe mmayembekezera inu komaso ife.
Tikuthokoza nonse chifukwa cha sapoti yomwe mmatipasa ndipempho lathu kuti mpitilize kutipasa sapotiπ
Lero zativuta π
π
21/08/2026
FIRST DEFEAT
FULL TIME
Chizumulu 4-0 Jenda United
21/08/2026
80|
Chizumulu 4-0 Jenda United
21/08/2026
69|Chizumulu yaonjezera chigoli cha number 4
Chizumulu 4-0 Jenda United
21/08/2026
60|
Chizumulu 3-0 Jenda United
21/08/2026
SECOND HALF UNDERWAY
Chizumulu 3-0 Jenda United