02/09/2025
Babatunde sopano ndi Malawi
Osewera wa ku sogolo wa timu ya Fcb Nyasa Big Bullets Babatunde sopano ndi fulu mu dziko lino la Malawi.
Babatunde sopano walandila chiphaso cha uzika ndipo atha kupanga chilichonse ngati mzika ya Malawi kuphatikiza kutumikila timu ya dziko lino.
Babatunde atha kupezeka mu gulu la osewera omwe atenge mbali pa masewero awiri omwe timu yathu ya dziko lino isewere mwezi uno.
Pali chiyembekezo choti Pasuwa ayitana osewerayu kamba koti ndi amene akusogola zigoli mu league ya dziko lino komaso ndi ovomerezeka kusewera timu yathu ya dziko lino.
18/08/2025
Ma Timu a Man U ndi Chelsea ayi zikomo mwayamba bwino ndithu
17/08/2025
FULL TIME
CHILUMBA BARRACKS 0-5 BULLETS
Mighty Tigers 0-1 Silver Strikers
Kamuzu Barracks 3-1 Thondwe FC
Mzuzu City Hammers 7 (1) - (1) 6 Baka City
Blue Eagles 0 (5) - (4) 0 Songwe Border United
Babatunde wayamba mwa pa mwamba kwambiri pomwe akusogola zigoli mu pikisano wa FDH Cup pomwe wagolesa zigoli 4 mu masewero andime ya ma timu 32 ku Chitipa pomwe Fcb Nyasa Big Bullets imakumana ndi timu ya Chilumba barracks.
Babatunde anafuna kubwelesa chimwemwe kwa osatila timuyi ku Chitipa pomwe ndikoyamba timuyi kukasewera masewero ku Chitipa. Baba anagolesa chigoli choyamba asanabwele Chawanangwa Gumbo ndi chigoli chachiwiri.
Babatunde anafuna kwawonesa anawa kuti iye ndamene akusogola zigoli mu Super league pomwe anaonjezera china asanapite kopumila. chigawo chachiwiri Baba anabwelaso ndi kugolesa zigoli zina ziwiri.
For more updated follow Wa Mpira Sakwiya Tv
15/08/2025
Awa ndi osewera a Fcb Nyasa Big Bullets omwe anyamuka ulendo wa ku Chitipa komwe akukakumana ndi Chulumba barracks mumasewero a FDH.
SQUAD LIST
GOALKEEPERS
Richard Chimbamba
Austin Chirambo
Innocent Nyasulu
DEFENDERS
02. Yamikan Molongeni
03. Blessings Joseph
04. Blessings Mpokera
12. Dominic Musonda
21. Andrew Jovinalla
25. Edward Thengo
27. Henry Chivaya
31. Khumbo Banda
MIDFIELDERS
06. Frank Willard
07. Peter Banda
08. Mike Mkwate
17. Yankho Singo
19. Wongani Lungu
28. Paul Master
29. Chawanangwa Gumbo
ATTACKERS
09. Hassan Kajoke
11. Chikumbutso Salima
13. Ephraim Kondowe
14. Sean Mcbrams
18. Babatunde Adepoju
20. Maxwell Phodo
22. Lameck Ghamphani
32. Bright Munthali
Head Coach: Peter Mponda
14/08/2025
Fcb Nyasa Big Bullets ili pa msewu kulowela ku Chitipa.
Bullets yatenga osewera okwana 26 ndipo Bright Bweke Munthali osewera amene wapanga gwilizano wasopano ndi timuyi ali gulu lopita ku Chitipa
All the best ma timu nonse weekend iyi wakulu wina akuzisiya mu FDH Cup.
Follow Wa Mpira Sakwiya Tv