Mpunga wa TC11 komanso ufa, zikupezeka pa mtengo wabwino!
Tiyimbireni pa 0999232901
γ
Choyamba, Tidye
Quality foods for a hunger-free Malawi. Together, we fight hunger, malnutrition, and food shortages by providing quality food products β for a healthier Malawi.
Our Malawi, Our pride.
29/04/2026
Anzanu achangu zikuwayendera ndipo akuchitira umboni!
Gulani kapena kuyitanitsa wanu Ufa kapena Mpunga pa nambala iyi π
0 999 232 901
γ
Kwacha koma choyamba tidye!
Mpunga wa Kilombero, mma pack a 5kg ndi 2kg
Ufa wa gaiwa, gramil ndi oyera wama vitamins ndima Minerals mma pack a
5kg ndi 2kg
Chimanga cha Popcorn pack ya 500g
For orders and delivery:
Call on:
+265 999 23 29 01
fans
γ
Kwacha koma choyamba tidye!
Mpunga wa Kilombero, mtengo ndi:
5kg - k30,000
2kg - k12,000
Ufa wa gaiwa, gramil ndi oyera wama vitamins ndima Minerals uliponso.
Mtengo:
5kg k10,500
2kg k4,500
Chimanga Popcorn, mtengo ndi:
500g - k4,000
For orders and delivery:
Call on:
+265 999 23 29 01
γ
Mpunga okoma wa TC 11 Kilombero ukupezeka.
Tiyimbireni pa 0999232901
16/02/2026
Kodi munaulawa mpunga wa TC11 Kilombero?
Tatiuzeni ndemanga yanu mu vomment section?
γ
14/02/2026
Kuli masewera atsikana achitanyu pa Bingu Stadium masanawa pakati pa Malawi U-20 ndi Guinea Bissau
Mpirawu ndiwa ulele koma nkutheka mufuna
Popcorn
Mpunga
Ufa
Apa mwayandikira kuchimake kopezeka katunduyu wa TC 11
Tiyankhuleni pa 0 999 232 901
γ
13/02/2026
Ndika mvula kameneka popcorn angakometu kumwera chai βοΈπΏ
500g ali pa k4,000 yokha basi.
Tiyankhuleni pa 0999 232 901
γ
13/02/2026
Awatu adya!
Alipo samafuna kudya?
Ndi k12,000 (2kg) kapena k30,000 (5kg) m***a kupeza wanu.
Tiyimbireni pa nambala iyi π
0 999 232 901
γ
Click here to claim your Sponsored Listing.
Location
Website
Address
GULLIVERAREA49