27/08/2026
Caf Women's Champions League Semifinal
Zesco Ndola girls imawona ngati sikucha iphodedwa lero
Silver Strikers ladies ๐ Zesco Ndola girls
๐๐ฑ๐ฉ๐๐ซ๐ข๐๐ง๐๐ ๐ญ๐ก๐ ๐ญ๐ก๐ซ๐ข๐ฅ๐ฅ ๐จ๐ ๐ฅ๐ข๐ฏ๐ ๐๐จ๐จ๐ญ๐๐๐ฅ๐ฅ ๐ฐ๐ข๐ญ๐ก ๐๐๐ฅ๐๐ฐ๐ข ๐๐ฉ๐จ๐ซ๐ญ๐ฌ ๐๐๐๐! ๐๐จ๐ข๐ง ๐จ๐ฎ๐ซ ๐๐จ๐ฆ๐ฆ๐ฎ๐ง๐ข๐ญ๐ฒ ๐๐จ๐ซ ๐ฆ๐๐ญ๐๐ก ๐ฎ๐ฉ๐๐๐ญ๐๐ฌ, ๐ฌ๐๐จ๐ซ๐๐ฌ, ๐๐ง๐ ๐ฌ๐ฉ๐จ๐ซ๐ญ๐ฌ ๐๐ข๐ฌ๐๐ฎ๐ฌ๐ฌ๐ข๐จ๐ง.
27/08/2026
Caf Women's Champions League Semifinal
Zesco Ndola girls imawona ngati sikucha iphodedwa lero
Silver Strikers ladies ๐ Zesco Ndola girls
26/08/2026
Kwangotsala masiku atatu Kodi inu mwagula kale
26/08/2026
Silver Strikers ladies ili ndime ya Semifinal ku mpikisano wa Cosafa Women's Championship pomwe mawa osewera ndi Zesco Ndola girls pofuna kudzigulura malo mu ndime yotsiliza
25/08/2026
Nsingizini HotSpurs yaphodedwa komaso ayisandutsa banker
Silver Strikers ladies 5-1 Nsingizini HotSpurs
25/08/2026
According to Twaha Chimuka striker John mchema has terminated his employment contract with Kamuzu Barracks FC to join Ekhaya FC and is expected to get a sum of 10 million Kwacha as signing on fee
25/08/2026
Bungwe la Super League of Malawi (SULOM) lati lamaliza kulandira ma umboni pazazomwe zidachitika pamasewero a Creck Sporting Club ndi Ekhaya FC ndipo lati lipereka chigamulo posachedwapa.
Masewero atatha kudali kusinthana zibakera pakati pa akulu akulu a timu ya Ekhaya komaso Creck Sporting Club
25/08/2026
Nduna ya zamasewero mdziko la South Africa Gayton McKenzie yalembera kalata bungwe loyendetsa mpira dzikolo la South African Football Association (SAFA) kuti libweze ndalama zokwana 13 million rand zomwe lidalandira Kuti libweretse makina aja a video assistant referee (VAR).
McKenzie wati ndi okhumudwa ndi SAFA kuti sidakwanilitse kubweletsa VAR mu ligi ya mdziko la South Africa ndipo wapeleka masiku 21 kuti SAFA ibweze ndalamazi.
Ndipo McKenzie ati adalembera kale kalata bungwe la FIFA kuti liwathandize kubweletsa VAR mu mdziko la South Africa
24/08/2026
Timu ya Silver Strikers ladies dzulo yagonja ndi zigoli zitatu kwa duu ndi timu ya Mamelodi Sundowns.
Koma the central bankers ili ndi umwayi ofika Semifinal ngati izagonjetse Nsingizini HotSpurs lachiwiri lino
23/08/2026
Yanuyo yokondwedwayo ili pati
23/08/2026
FDH Bank Premiership results today