22/07/2026
Yanuyo ili pati
Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from KUMA STAND, Sport & recreation, Chilomoni, Blantyre.
KUMA STAND is a proffessional Sports and recreation Page which covers all sports News and live Broadcast from several Major Stadiums across Malawi and The whole world, this includes...
Fixtures,live Results, KUMA STAND PODCAST, and Transfer Update
22/07/2026
Yanuyo ili pati
A Ref nthawiðŸ¤
22/04/2026
Week yoyambira tikhala tili mabwalo amenewa kuchitira umboni mene masapota Atamwele wamkaka onsiyanasiyana muno mmalawi ndikutitu inu mu FDH BANK premiership....
18/04/2026
Ife chete kudikila yowinayo timbwembwedzere tizipita Stand yomwe ikukomayo koma inu pa Stand pa
Manoma nde akuti ailandira Bata muchaka cha 2026 akufuna amalizise pomwe aasiira hhhmmm
pa Stand lero pachema
Tinapanga kaye zii pakatipa kuti tikoze pena ndi pena league isanayambe chifukwa chaka chino zilikotu
Ndikuti Kwangosalatu Mwenzi umodzi okha Bwede chikadzat.....
25/03/2026
Mndandanda wa Anyamata osewera mpira wa miyendo wa dziko lino okwana 25 Omwe akukatenga nawo gawo mumpikisano wa 4 NATIONALS TOURNAMENT mu mzinda wa Francis town ku Botswana kuyambira pa 28 mpaka pa 31 March chaka chino Watuluka.
Kuno monga ife kwanthu ndikuichemelera yamotoyi kuti Chinthuchi tibwele nacho kuno kumudzi🔥🔥🔥🔥🇲🇼🇲🇼🇲🇼