Ndindani Kodi Pa dengapo? Utanipo thawi zino?
Zikomo Social Net
Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from Zikomo Social Net, Sport & recreation, United States International University/Africa, Nairobi.
Zikomo Social Net | Home of Infotainment ๐ฌ๐ฅ
Where creativity meets purpose โ promoting talent, stories & brands that inspire change.
๐ +265 991 440 060 / +254 748 437 887
Musakudziwa muja muli mtendere
๐ญ๐
08/08/2026
Apolisi ati atenga njira zokhwima polimbana ndi anthu omwe amachita nkhanza zogonana ndi ana, zomwe zikupitilizabe kusokoneza komanso kulanda ufulu wa ana.
Polankhula lero pa Sexual Violence Awareness Pool Bonanza yomwe yachitikira ku Mchinji, Officer In-Charge wa Mchinji Police Station, Dr. David Pheremero Kumwenda, ati anthu omwe apezeka ndi mlanduwu akuyembekezera zilango zokhwima za kundende, pofuna kuletsa ena kuti asamachite nkhanza zotere.
Dr. Kumwenda wapemphanso anthu onse kuti atenge nawo mbali poteteza ana, makamaka kufotokozera apolisi kapena akuluakulu oyenera akazindikira kapena kukayikira kuti mwana akuchitiridwa nkhanza.
Pakadali pano, Regional Executive Committee Chairperson wa Central West Police Region, Dr. Alex Chapondera, walonjeza kuti agwira ntchito limodzi ndi apolisi pothandiza kulimbikitsa chitetezo cha ana ku nkhanza.
Malinga ndi polisi ya Mchinji yalandira milandu 37 ya nkhanza zogonana ndi ana kuyambira January mpaka June 2026, poyerekeza ndi milandu 22 yomwe idanenedwa nthawi yomweyi mu 2025.
Izi zikutanthauza kuti milanduyi yakwera ndi 15 poyerekeza ndi chaka chatha.
๐ก๏ธ Ana ndi tsogolo lathu. Tiyeni tonse titenge nawo mbali powateteza. Ngati mukudziwa kapena mukukayikira nkhanza, nenani kwa apolisi kapena akuluakulu oyenera.
Picture : Zodiak Online (Blessings Kang'ombe)Mike Mangani Chills Sport and Mchinji PRO
Full Time
Mchinji Villa 1-1 Mchinji Boma Strikers
/MchinjiDerby
08/08/2026
08/08/2026
Late MBC Director General Brian Banda will be laid to rest on Monday, August 10, 2026, at Mโbanda Village, Chileka.
Mchinji People
Mukamvako munthu akugulitsa HP laptop grey in color, phone itel, Mattress a red, sound bar (D jack), JBL speaker ya red....
Chonde ndidziwitseniko andibela ma staff houses...
0884560783
0996099096 (Nellie Pulumuka)
MG2 Mpaka kugonera futali osangozi Siya bwanj? ๐
Mukatumiza ana ku holiday sizowafusa mwadya chani
Siku hotel kuno๐๐
08/08/2026
โ76Minutes zathapo
๐PSG 1-1 MAN U
Click here to claim your Sponsored Listing.
Location
Category
Telephone
Website
Address
Nairobi
00800