Timveni News Updates360

Timveni News  Updates360

Compartir

DAILY NEWS
HOME FOR ENTERTAINMENT
BRINGING HOPE TO EVERY FOLLOWER
🔥🔥🔥🔥🔥💪💪💪💪👇👇👇

19/06/2026

ADMIN ATHU LERO NDI GRADUATION YAWO I WISH ALL THE BEST TO HIM💪💪💪

11/06/2026

ZOMWE MUYENELA KUDZIWA ZA FIFA WORLD CUMP 2026

1 . Kwa nthawi yoyamba ma team akhalapo 48 osati 32 . Masewelo azaponyedwa ka 104 Malo mwa 64 .

2 .Mayiko atatu USA , Mexico ndi Canada agwila ntchito limodzi kwa nthawi yoyamba

3 . Masewelo ambili achitikila ku Texas , Arizona ndi Mexico masana . Madela awa amatetha kwambili moti kuthetha ku mafika 45⁰C

4 . Stadium yotetha kwambili ndi AT yomwe ili ku Texas . Inapangidwa ngati food wormer yoyikamo nsima . Nde chikati chitethe chimatethadi zeni zeni

5 . Masewelo ena 16 akachitikila ku Mexico. Mu mbili ya FIFA . Mexico idzakhala dziko loyamba kuchitisa World cup katatu mu 1970, 1986 ndi 2026 . Komaso Canada kakhala loyamba

6 . Final idzakhala ku New Jersey osati New York.

7 . FIFA igwilisa ntchito makina a AI ndi VAR amakono . Omwe azijambula ma offside kuyambila nthupi la munthu

8 . Akuba nawo avuta ku USA , Canada ndi Mexico. Akumaba ndalama za anthu pa ATM komaso akupanga ma tickets aboza

9 . Masewelo a lran vs USA komaso USA vs Mexico. Kuzakhala asilikali ankhondo ambili . Mayiko awa Ali pa udani wanyoo...

10 . Ma hotel akwela ku USA . Ku choka pa 500 dollar to 1000 dollar pa usiku umodzi . Yomwe kwathu kuno ndi ndalama yopitilila 1.2 million. Anthu ambili agona ma galimoto

11. FIFA yasitha Chikho kapangidwe kake. Achichosa Chifukwa ena amati chinali ndi mawonekedwe a njoka . Zomwe amati ndi za satanic

Tipitilize or tisiyile popa
⚽⚽⚽⚽⚽⚽⚽
Martial Focus

11/06/2026

BREAKING NEWS

UEFA has announced that the Somali referee Omar Artan will officiate the UEFA Super Cup match between PSG and Aston Villa in Salzburg.

This comes barely days after he was denied entry into United States of America to officiate matches at the 2026 World Cup.

News Updates #
Timveni News Updates360

11/06/2026

Court la Magistrate ku Ntchisi lapeza kuti bambo Grecian Sandram azaka 35 ndiosalakwa pa mulandu ogwilira mtsikana wa zaka 15 omwe amawaganizila.

Azachipatala anapeleka umboni onena kuti atamuyeza mtsikana yi samapeze umboni uliwonse kuti analowetsedwa kanthu. Komanso mtsikana yi mu umboni wake anakanika kunena kuti Grecian anamugwilira kutiko
Wolemba:Timveni News Updates360
me please #

10/06/2026



A polisi amanga anthu atatu kamba kopezeka ndi chamba chosavomerezeka kwa Chemusa ku Blantyre.

Othandizira mneneri wa apolisi ku Blantyre, a Doris Mwitha, wati atatuwa ndi a Loy Chinangwa, a Hanif Vasilatosi ndi a Benard Saiwala.

A Mwitha ati apolisi alanda chambachi ndipo anthuwa akaonekera ku bwalo la milandu posachedwa.

(by Chikondi Mphande-Blantyre:06/10/26)

10/06/2026



Former Ntcheu Central Constituency Member of Parliament and First Deputy Speaker of Parliament, Hon. Jones Chingola, has died this morning at Kamuzu Central Hospital in Lilongwe after a long illness.

The late Chingola's son, Jones Chingola Jnr, says his father had been suffering from stroke, diabetes, and high blood pressure since 2012 until his death.

He says arrangements are currently underway to transfer the body to Mthunzi Mortuary, pending transportation to his home village in Ntcheu District tomorrow.

Chingola Jnr adds that the burial ceremony is expected to take place on Friday.

The late Hon. Jones Chingola served as Member of Parliament for Ntcheu Central Constituency and as First Deputy Speaker of Parliament from 2009 to 2014.
Timveni News Updates360
#
SOURCE:Zodiak Online

Photos from Timveni News  Updates360's post 10/06/2026

Shenzhen Bao'an International Airport ili ku Guangdong, China ndipo ndi imodzi mwa ma airport otanganidwa kwambiri padziko lapansi!

Terminal yachitatu anaipanga ngati msomba ya manta ray ndiyayitali 1.5km ,
Ili ndi runway yomangidwa m'nyanja gawo lina limamangidwa pamadzi,
Imalumikizidwa ndi bullet train ukatsika ndege ukhoza kukwera sitima nthawi yomweyo .
Timveni News Updates360
#

¿Quieres que tu empresa sea el Gimnasio mas cotizado en Madrid?

Haga clic aquí para reclamar su Entrada Patrocinada.

Localización

Página web

Dirección

Post Office Box 28
Madrid